Yoswa 18:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo amunawo ananyamuka, namuka; ndipo Yoswa analamulira opita kulemba dzikowo, ndi kuti, Mukani, muyendeyende pakati padziko, ndi kulilemba, nimubwerenso kwa ine, ndipo ndidzakuloterani maere pano pamaso pa Yehova pa Silo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo amunawo ananyamuka, namuka; ndipo Yoswa analamulira opita kulemba dzikowo, ndi kuti, Mukani, muyendeyende pakati pa dziko, ndi kulilemba, nimubwerenso kwa ine, ndipo ndidzakuloterani maere pano pamaso pa Yehova pa Silo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono anthuwo adapitadi kukalemba za dzikolo, Yoswa ataŵalangiza kuti, “Pitani, kaliyendereni dziko lonselo, ndipo mukalembe bwino za dzikolo. Tsono mutatero, mubwererenso kwa ine kuno. Ine ndidzakuchitirani maere pamaso pa Chauta konkuno ku Silo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Anthuwo akupita kukalembera dzikolo, Yoswa anawalangiza kuti, “Pitani mukayendere ndi kulembera dzikolo. Kenaka mukabwere kwa ine, ndidzakuchitirani maere kuno ku Silo pamaso pa Yehova.” Onani mutuwo |