Yoswa 18:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anatsala mwa ana a Israele mafuko asanu ndi awiri osawagawira cholowa chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anatsala mwa ana a Israele mafuko asanu ndi awiri osawagawira cholowa chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Nthaŵi imeneyo nkuti mafuko asanu ndi aŵiri asanapatsidwe magawo ao a dzikolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma pa nthawiyo nʼkuti mafuko asanu ndi awiri a Aisraeli asanalandire cholowa chawo. Onani mutuwo |