Yoswa 17:9 - Buku Lopatulika9 Natsikira malire ku mtsinje wa Kana, kumwera kwa mtsinje; mizinda iyi inakhala ya Efuremu pakati pa mizinda ya Manase; ndi malire a Manase anali kumpoto kwa mtsinje; ndi matulukiro ake anali kunyanja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Natsikira malire ku mtsinje wa Kana, kumwera kwa mtsinje; midzi iyi inakhala ya Efuremu pakati pa midzi ya Manase; ndi malire a Manase anali kumpoto kwa mtsinje; ndi matulukiro ake anali kunyanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono malire ake adatsikira ku kamtsinje ka Kana. Mizinda yakumwera kwa kamtsinje kameneka inali ya fuko la Efuremu, ngakhale inali m'dziko la Manase. Malire a dziko la Manase adalambalala chakumpoto kwa kamtsinjeko, nakalekezera ku nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo malire ake anapitirira kummwera mpaka ku mtsinje wa ku Kana. Mizinda ya kummwera kwa mtsinjewo inali ya fuko la Efereimu ngakhale kuti inali mʼdziko la Manase. Malire a fuko la Manase anapita kumpoto kwa mtsinje wa Kana ndi kukathera ku Nyanja. Onani mutuwo |