Yoswa 17:8 - Buku Lopatulika8 Dziko la Tapuwa linali la Manase; koma Tapuwa mpaka malire a Manase linakhala la ana a Efuremu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Dziko la Tapuwa linali la Manase; koma Tapuwa mpaka malire a Manase linakhala la ana a Efuremu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Dzikolo linali la Manase, koma mzinda wa Tapuwa wapamalire unali wa fuko la Efuremu, ngakhale kuti m'pakati penipeni pa mizinda ya Manase. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 (Manase anatenga dziko la Tapuwa, koma mzinda wa Tapuwawo, umene unali mʼmalire mwa Manase unali wa fuko la Efereimu). Onani mutuwo |