Yoswa 17:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anayandikira pamaso pa Eleazara wansembe, ndi pamaso pa Yoswa mwana wa Nuni, ndi pamaso pa akalonga, ndi kuti, Yehova analamulira Mose atipatse cholowa pakati pa abale athu; chifukwa chake anawapatsa monga mwa lamulo la Yehova, cholowa pakati pa abale a atate wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anayandikira pamaso pa Eleazara wansembe, ndi pamaso pa Yoswa mwana wa Nuni, ndi pamaso pa akalonga, ndi kuti, Yehova analamulira Mose atipatse cholowa pakati pa abale athu; chifukwa chake anawapatsa monga mwa lamulo la Yehova, cholowa pakati pa abale a atate wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Iwoŵa adabwera kwa Eleazara wansembe, nafikanso kwa Yoswa mwana wa Nuni ndi kwa atsogoleri, ndipo adati, “Chauta adalamula Mose kuti ife ndi alongo athu atipatse gawo lina la dziko ngati choloŵa chathu.” Motero iwowo, pamodzi ndi abale a bambo wao, adapatsidwa dziko kuti likhale lao potsata zimene Chauta adalamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo anapita kwa Eliezara wansembe, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri ndipo anati: “Yehova analamula Mose kuti ife ndi alongo athu atipatse cholowa chathu.” Choncho iwowo pamodzi ndi abale a abambo awo anawapatsa dera lina la dzikolo kuti likhale monga mwa lamulo la Yehova. Onani mutuwo |