Yoswa 17:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo maere anagwera ana ena otsala a Manase monga mwa mabanja ao; ana a Abiyezere ndi ana a Heleki, ndi ana a Asiriele, ndi ana a Sekemu ndi ana a Hefere, ndi ana a Semida; awa ndi ana aamuna a Manase mwana wa Yosefe, monga mwa mabanja ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo maere anagwera ana ena otsala a Manase monga mwa mabanja ao; ana a Abiyezere ndi ana a Heleki, ndi ana a Asiriele, ndi ana a Sekemu ndi ana a Hefere, ndi ana a Semida; awa ndi ana amuna a Manase mwana wa Yosefe, monga mwa mabanja ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mabanja otsala a Manase amene adapatsidwanso dziko ndi aŵa: Abiyezere, Heleki, Asiriele, Sekemu, Hefere ndi Semida. Ameneŵa ndiwo zidzululu za Manase, mwana wa Yosefe, komanso ndiwo amene anali eni mbumba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Mabanja ena otsala a fuko la Manase amene analandira dziko ndi awa: Abiezeri, Heleki, Asirieli, Sekemu, Heferi ndi Semida. Izi ndi zidzukulu zina zazimuna za Manase mwana wa Yosefe ndiponso eni mbumba. Onani mutuwo |