Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 16:9 - Buku Lopatulika

9 pamodzi ndi mizinda adaipatulira ana a Efuremu pakati pa cholowa cha ana a Manase, mizinda yonse pamodzi ndi midzi yao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 pamodzi ndi midzi adaipatulira ana a Efuremu pakati pa cholowa cha ana a Manase, midzi yonse pamodzi ndi milaga yao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 kuphatikizapo mizinda ndi midzi yopatsidwa kwa Aefuremu, koma yokhala m'kati mwa dziko la anthu a fuko la Manase.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 kuphatikizapo mizinda yonse ndi midzi yake yopatsidwa kwa Efereimu, koma yokhala mʼkati mwa dziko la Manase.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 16:9
6 Mawu Ofanana  

namlonga ufumu wa pa Giliyadi ndi Aasiriya ndi Yezireele ndi Efuremu ndi Benjamini ndi Aisraele onse.


Ndipo dziko lao, ndi pokhala pao ndizo Betele ndi midzi yake, ndi kum'mawa Naarani, ndi kumadzulo Gezere ndi midzi yake, ndi Sekemu ndi midzi yake, mpaka Aya ndi midzi yake;


Ndi m'malire a Manase, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Efuremu, limodzi.


Ndipo sanaingitse Akanani akukhala mu Gezere; koma Akanani anakhala pakati pa Efuremu, kufikira lero lino, nawaumiriza kugwira ntchito yathangata.


Kuyambira ku Tapuwa malire anamuka kumadzulo ku mtsinje wa Kana; ndi matulukiro ake anali kunyanja. Ichi ndi cholowa cha fuko la ana a Efuremu monga mwa mabanja ao;


Natsikira malire ku mtsinje wa Kana, kumwera kwa mtsinje; mizinda iyi inakhala ya Efuremu pakati pa mizinda ya Manase; ndi malire a Manase anali kumpoto kwa mtsinje; ndi matulukiro ake anali kunyanja;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa