Yoswa 16:3 - Buku Lopatulika3 natsikira kumadzulo kunka ku malire a Ayafileti, ku malire a Betehoroni wa kunsi, ndi ku Gezere; ndi matulukiro ake anali kunyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 natsikira kumadzulo kunka ku malire a Ayafileti, ku malire a Betehoroni wa kunsi, ndi ku Gezere; ndi matulukiro ake anali kunyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono lidapitirira ndithu kuzambwe, kudera la Ayafaleti, mpaka kufika kunsi kwa Betehoroni. Kuchokera kumeneko malire ake adalunjika ku Gezere, nakalekeza mpaka ku nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Malirewo anatsikira cha kumadzulo kwa dziko la Yafuleti mpaka ku chigawo cha kumunsi kwa Beti-Horoni. Kuchokera kumeneko anapitirira mpaka ku Gezeri nʼkuthera ku Nyanja. Onani mutuwo |