Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 16:2 - Buku Lopatulika

2 natuluka ku Betele kunka ku Luzi, napitirira kunka ku malire a Aariki, ku Ataroti;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 natuluka ku Betele kunka ku Luzi, napitirira kunka ku malire a Aariki, ku Ataroti;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Kuchokera ku Betele malire ake adakafika ku Luzi, nabzola ku Ataroti kumene kunkakhala Aaraki.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Kuchokera ku Beteli malire ake anakafika ku Luzi, kudutsa dziko la Ataroti kumene kumakhala Aariki.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 16:2
8 Mawu Ofanana  

Ndipo anatcha dzina la pamenepo Betele; pakuyamba dzina lake la mzindawo ndi Luzi.


Ndipo kunali pakufika Davide ku mutu wa phiri, kumene amapembedza Mulungu, onani, Husai Mwariki anadzakomana naye ali ndi malaya ake ong'ambika, ndi dothi pamutu pake.


Chomwecho Husai bwenzi la Davide anadza m'mzindamo; ndipo Abisalomu anafika ku Yerusalemu.


Ndipo kunali pakudza kwa Abisalomu Husai Mwariki, bwenzi la Davide, Husai ananena ndi Abisalomu, Mfumu ikhale ndi moyo. Mfumu ikhale ndi moyo.


ndi Ahitofele anali phungu wa mfumu, ndi Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu;


Ndipo dziko lao, ndi pokhala pao ndizo Betele ndi midzi yake, ndi kum'mawa Naarani, ndi kumadzulo Gezere ndi midzi yake, ndi Sekemu ndi midzi yake, mpaka Aya ndi midzi yake;


Ndipo malire anapitirirapo kunka ku Luzi, ku mbali ya Luzi, momwemo ndi Betele, kumwera; ndi malire anatsikira kunka ku Ataroti-Adara, kuphiri lokhala kumwera kwa Betehoroni wa kunsi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa