Yoswa 16:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo gawo la ana a Yosefe linatuluka kuchokera ku Yordani ku Yeriko, ku madzi a Yeriko kum'mawa, kuchipululu, nakwera kuchokera ku Yeriko kunka kumapiri ku Betele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo gawo la ana a Yosefe linatuluka kuchokera ku Yordani ku Yeriko, ku madzi a Yeriko kum'mawa, kuchipululu, nakwera kuchokera ku Yeriko kunka kumapiri ku Betele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Dziko limene lidapatsidwa kwa zidzukulu za Yosefe lidayambira ku mtsinje wa Yordani pafupi ndi Yeriko, cha kuvuma kwa akasupe a Yeriko, kukaloŵa m'chipululu. Lidayambiranso ku Yeriko, ndi kukaloŵa m'dziko lamapiri chakuzambwe, mpaka kukafika ku chipululu cha Betele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Dziko limene linapatsidwa kwa fuko la Yosefe linayambira ku mtsinje wa Yorodani ku Yeriko, kummawa kwa akasupe a Yeriko, ndiponso kuyambira mtsinje wa Yorodaniwo nʼkumakwera, kudutsa mʼchipululu mpaka ku mapiri a ku Beteli. Onani mutuwo |