Yoswa 15:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo analemba malire kuyambira pamwamba paphiri mpaka chitsime cha madzi cha Nefitowa, natulukira malire kumizinda ya phiri la Efuroni; ndipo analemba malire kunka ku Baala, ndiwo Kiriyati-Yearimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo analemba malire kuyambira pamwamba pa phiri mpaka chitsime cha madzi cha Nefitowa, natulukira malire kumidzi ya phiri la Efuroni; ndipo analemba malire kunka ku Baala, ndiwo Kiriyati-Yearimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono adachokeranso pamwamba pa phiri, nakafika mpaka ku akasupe a Nepitowa, nadzatulukira ku mizinda ya ku phiri la Efuroni. Kuchoka uko nkutsikira ku Baala, (ndiye kuti Kariyati-Yearimu), Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo anachokeranso pamwamba pa phiri, kukafika mpaka ku akasupe a ku Nepitowa, nadzatulukira ku mizinda ya phiri la Efroni, ndi kutsikira ku Baalahi (ndiye Kiriati Yearimu). Onani mutuwo |