Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 15:6 - Buku Lopatulika

6 nakwera malire kunka ku Betehogila, napitirira kumpoto kwa Betaraba; nakwera malire kunka ku mwala wa Bohani mwana wa Rubeni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 nakwera malire kunka ku Betehogila, napitirira kumpoto kwa Betaraba; nakwera malire kunka ku mwala wa Bohani mwana wa Rubeni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 napitirira mpaka ku Betehogila, nakafika kumpoto kwa Betaraba. Adapitirira mpaka kukafika ku Mwala wa Bohani, mwana wa Rubeni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 napitirira mpaka ku Beti-Hogila ndi kupitirira kumpoto mpaka ku Beti-Araba. Anapitirira mpaka anakafika ku Mwala wa Bohani.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 15:6
5 Mawu Ofanana  

Ndi malire a kum'mawa ndiwo Nyanja ya Mchere, mpaka mathiriro ake a Yordani. Ndi malire a kumpoto anayambira nyondo ya nyanja ku mathiriro a Yordani;


M'chipululu, Betaraba, Midini, ndi Sekaka;


nakwera malire kunka ku Debiri, kuchokera ku chigwa cha Akori, ndi kumpoto kupenyera Giligala ndiko kundunji kwa chikweza cha Adumimu, ndiko kumwera kwa mtsinje; napitirira malire kunka ku madzi a Enisemesi, ndi matulukiro ake anali ku Enirogele;


nalembedwa kunka kumpoto, natuluka ku Enisemesi, natuluka ku Geliloti, ndiwo pandunji pokwerera pa Adumimu; natsikira ku mwala wa Bohani mwana wa Rubeni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa