Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 15:41 - Buku Lopatulika

41 ndi Gederoti, Betedagoni, ndi Naama, ndi Makeda; mizinda khumi ndi isanu ndi umodzi pamodzi ndi midzi yao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 ndi Gederoti, Betedagoni, ndi Naama, ndi Makeda; midzi khumi ndi isanu ndi umodzi pamodzi ndi milaga yao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Gederoti, Betedagoni, Naama ndiponso Makeda. Yonse inali mizinda 16, pamodzi ndi midzi yake yozungulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Gederoti, Beti-Dagoni, Naama ndi Makeda. Mizinda yonse pamodzi inalipo 16 pamodzi ndi midzi yake yozungulira.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 15:41
10 Mawu Ofanana  

ndi woyang'anira mitengo ya azitona, ndi yamikuyu yokhala kuzidikha kunsi, ndiye Baala-Hanani Mgederi; ndi woyang'anira zosungiramo mafuta ndiye Yowasi;


Afilisti omwe adagwa m'mizinda ya kuchidikha, ndi ya kumwera kwa Yuda, nalanda Betesemesi, ndi Ayaloni, ndi Gederoti, ndi Soko ndi midzi yake, ndi Timna ndi midzi yake, ndi Gimizo ndi midzi yake; nakhala iwo komweko.


Atamva tsono mabwenzi atatu a Yobu za choipa ichi chonse chidamgwera, anadza, yense kuchokera kwao, Elifazi wa ku Temani, ndi Bilidadi Msuki, ndi Zofari wa ku Naama, napangana kudzafika kumlirira ndi kumsangalatsa.


Ndipo Yehova anawamwaza pamaso pa Israele, ndipo anawakantha makanthidwe aakulu ku Gibiyoni, nawapirikitsa panjira yokwera pa Betehoroni, nawakantha mpaka Azeka, ndi mpaka Makeda.


anthu onse anabwerera kuchigono kwa Yoswa pa Makeda ndi mtendere. Palibe munthu anachitira chipongwe mmodzi yense wa ana a Israele.


Ndipo Yoswa anagwira Makeda tsiku lomwe lija ndi kuukantha ndi lupanga lakuthwa, ndi mfumu yake yomwe; anawaononga konse, ndi amoyo onse anali m'mwemo, osasiyapo ndi mmodzi yense, nachitira mfumu ya ku Makeda monga anachitira mfumu ya ku Yeriko.


mfumu ya ku Makeda, imodzi; mfumu ya ku Betele, imodzi;


ndi Kaboni, ndi Lahamasi, ndi Kitilisi;


Libina ndi Eteri ndi Asani;


nazungulira kotulukira dzuwa ku Betedagoni, nafikira ku Zebuloni ndi ku chigwa cha Ifutahele, kumpoto ku Betemeke, ndi Neiyeli; natulukira ku Kabulu kulamanzere,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa