Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 15:3 - Buku Lopatulika

3 natuluka kumwera kwa chikweza cha Akarabimu, napitirira ku Zini, nakwera kumwera kwa Kadesi-Baranea, napitirira ku Hezironi, nakwera ku Adara, nazungulira ku Karika;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 natuluka kumwera kwa chikweza cha Akarabimu, napitirira ku Zini, nakwera kumwera kwa Kadesi-Baranea, napitirira ku Hezironi, nakwera ku Adara, nazungulira ku Karika;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 napita cha kumwera kokhakokha kuyambira ku chikweza cha ku Akarabimu, nkudzera pa mpata wa mapiri a ku Zini. Kuchokera kumeneko, adabzola cha kumwera kwa Kadesi-Baranea, kupitirira Hezironi mpaka ku Adara, ndi kutembenukira ku Karaka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 kudutsa cha kummwera ku Akirabimu, nʼkupitirira mpaka ku Zini. Kuchokera pamenepo nʼkumapita cha kummwera kwa Kadesi Barinea, kudutsa Hezironi mpaka ku Adari ndi kutembenuka mpaka ku Karika.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 15:3
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anabwera nafika ku Enimisipati (kumeneko ndi ku Kadesi), nakantha dziko lonse la Aamaleke, ndiponso Aamori amene akhala mu Hazazoni-Tamara.


Ndipo ana a Israele, ndilo khamu lonse, analowa m'chipululu cha Zini mwezi woyamba; ndipo anthu anakhala mu Kadesi; kumeneko anafa Miriyamu, naikidwa komweko.


Anatero makolo anu, muja ndinawatumiza achoke ku Kadesi-Baranea kukaona dziko.


ndi malire anu adzapinda kuchokera kumwera kunka pokwera Akarabimu, ndi kupitirira ku Zini; ndi kutuluka kwake adzachokera kumwera ku Kadesi-Baranea, nadzatuluka kunka ku Hazara-Adara, ndi kupita kunka ku Azimoni;


Ndi malire ao a kumwera, anayambira ku malekezero a Nyanja ya Mchere, ku nyondo yoloza kumwera;


napitirira ku Azimoni, natuluka ku mtsinje wa Ejipito; ndi malekezero a malirewa anali ku Nyanja Yaikulu; awa ndi malire anu a kumwera.


Ndipo malire a Aamori anayambira pokwerera pa Akarabimu, pathanthwe ku Sela, ndi pokwererapo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa