Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 13:10 - Buku Lopatulika

10 ndi mizinda yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori, wakuchita ufumu mu Hesiboni, mpaka malire a ana a Amoni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 ndi midzi yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori, wakuchita ufumu m'Hesiboni, mpaka malire a ana a Amoni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Linkaphatikizaponso mizinda yonse yomwe inkalamulidwa ndi Sihoni mfumu ya Aamori, amene ankalamula ku Hesiboni, mpaka ku malire a Aamoni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Linkaphatikizanso mizinda yonse ya mfumu Sihoni ya Aamori, imene inkalamulira mu Hesiboni, mpaka ku malire a Aamoni.

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 13:10
5 Mawu Ofanana  

atakantha Sihoni mfumu ya Aamori, wakukhala mu Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basani, wakukhala mu Asitaroti, ku Ederei.


Ndipo pamene uyandikiza popenyana ndi ana a Amoni, usawavuta, kapena kuutsana nao; popeza sindidzakupatsako dziko la ana a Amoni likhale lakolako; popeza ndinapatsa ana a Loti ili likhale laolao.


ndi Giliyadi, ndi malire a Agesuri, ndi Amaakati, ndi phiri lonse la Heremoni, ndi Basani lonse mpaka ku Saleka;


kuyambira pa Aroere, wokhala m'mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndi mzinda uli pakati pa chigwa, ndi chidikha chonse cha Medeba mpaka ku Diboni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa