Yoswa 13:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Yoswa anakalamba, wa zaka zambiri; ndipo Yehova ananena naye, Wakalamba, wa zaka zambiri, ndipo latsala dziko lalikulukulu, alilandire cholowa chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Yoswa anakalamba, wa zaka zambiri; ndipo Yehova ananena naye, Wakalamba, wa zaka zambiri, ndipo latsala dziko lalikulukulu, alilandire cholowa chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Nthaŵi imeneyo Yoswa anali atakalamba kwambiri. Tsono Chauta adamuuza kuti, “Tsopanotu iwe wakalamba kwambiri, koma dziko losalandidwa likalipo lalikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yoswa atakalamba Yehova anamuwuza kuti, Iwe tsopano wakalamba kwambiri, koma dziko losalandidwa lilipobe lalikulu. Onani mutuwo |