Yoswa 12:9 - Buku Lopatulika9 mfumu ya ku Yeriko, imodzi; mfumu ya ku Ai, ndiwo m'mbali mwa Betele, imodzi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 mfumu ya ku Yeriko, imodzi; mfumu ya ku Ai, ndiwo m'mbali mwa Betele, imodzi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mafumu amene adagonjetsedwawo ndi aŵa: mafumu a ku Yeriko, Ai pafupi ndi Betele, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 mfumu ya Yeriko imodzi mfumu ya Ai (kufupi ndi Beteli imodzi Onani mutuwo |