Yoswa 12:4 - Buku Lopatulika4 Nalandanso malire a Ogi mfumu ya Basani wotsala wa Arefaimu, wokhala ku Asitaroti ndi ku Ederei, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Nalandanso malire a Ogi mfumu ya Basani wotsala wa Arefaimu, wokhala ku Asitaroti ndi ku Ederei, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Aisraele adagonjetsanso Ogi, mfumu ya ku Basani, amene anali mmodzi mwa otsala a Arefaimu. Iyeyu ankakhala ku Asitaroti ndi ku Ederei. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ogi mfumu ya mzinda wa Basani, amene anali mmodzi mwa otsala mwa Arefaimu. Iye ankakhala ku Asiteroti ndi Ederi. Onani mutuwo |