Yoswa 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Yoswa anawachitira monga Yehova adamuuza: nadula akavalo ao mitsindo, natentha magaleta ao ndi moto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Yoswa anawachitira monga Yehova adamuuza: nadula akavalo ao mitsindo, natentha magaleta ao ndi moto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Yoswa adangoŵachita zomwe Chauta adalamula. Adalumaza akavalo, natentha magaleta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yoswa anawachita zimene Yehova analamula. Iye anadula matsinde a akavalo awo ndi kutentha magaleta awo. Onani mutuwo |