Yoswa 11:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazori anachimva, anatuma kwa Yobabu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa mfumu ya ku Akisafu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazori anachimva, anatuma kwa Yobabu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa mfumu ya ku Akisafu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mbiri ya zimene zinkachitikazi idamfika Yabini, mfumu ya ku Hazori. Motero iyeyo adatumiza uthenga kwa Yobabu mfumu ya ku Madoni, ndiponso kwa mafumu a ku Simironi ndi Akisafu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yabini, mfumu ya Hazori, inamva zimene zinachitikazi. Tsono inatumiza uthenga kwa Yobabu mfumu ya Madoni, ndiponso kwa mafumu a ku Simironi ndi Akisafu. Onani mutuwo |