Yoswa 10:4 - Buku Lopatulika4 Kwerani kwanga kuno, ndi kundithandiza kuti tikanthe Gibiyoni, pakuti unachitirana mtendere ndi Yoswa ndi ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kwerani kwanga kuno, ndi kundithandiza kuti tikanthe Gibiyoni, pakuti unachitirana mtendere ndi Yoswa ndi ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Bwerani mudzandithandize kumenyana ndi Gibiyoni, chifukwa anthu ake apangana za mtendere ndi Yoswa ndiponso ndi Aisraele onse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iye anatumiza mawu kuti, “Bwerani mudzandithandize kumenyana ndi Gibiyoni, chifukwa anthu ake achita pangano la mtendere ndi Yoswa ndi Aisraeli.” Onani mutuwo |