Yoswa 1:18 - Buku Lopatulika18 Aliyense wakupikisana ndi inu, osamvera mau anu mulimonse mukamlamulira, aphedwe; komatu khalani wamphamvu, nimulimbike mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Aliyense wakupikisana ndi inu, osamvera mau anu mulimonse mukamlamulira, aphedwe; komatu khalani wamphamvu, nimulimbike mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Aliyense wokangana ndi inu kapena wosamvera malamulo anu, adzaphedwa. Inu mukhale amphamvu, ndipo mulimbe mtima kwambiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Aliyense wotsutsana ndi inu kapena wosamvera zimene mutilamula adzaphedwa. Inu mukhale wamphamvu ndi wolimba mtima!” Onani mutuwo |