Yoswa 1:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anamyankha Yoswa, nati, Zonse mwatilamulira tidzachita, ndipo kulikonse mutitumako tidzamuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anamyankha Yoswa, nati, Zonse mwatilamulira tidzachita, ndipo kulikonse mutitumako tidzamuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Onsewo adayankha Yoswa kuti, “Zonse zimene mwatilamulazi tidzachita, ndipo kulikonse kumene mudzatitume, tidzapita. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kenaka iwo anayankha Yoswa kuti, “Ife tidzachita chilichonse chimene mwatilamula, ndipo kulikonse kumene mudzatitume tidzapita. Onani mutuwo |