Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 1:13 - Buku Lopatulika

13 Kumbukirani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Kumbukirani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 “Kumbukirani zija zimene Mose, mtumiki wa Chauta, adakuuzani, kuti, ‘Chauta, Mulungu wanu, adzakupatsani dziko limeneli kuti likhale lanu.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 “Kumbukirani zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani kuti, ‘Yehova Mulungu wanu akukupatsani mpumulo, ndi dziko ili kuti likhale lanu.’

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 1:13
6 Mawu Ofanana  

Atero Yehova, Anthu opulumuka m'lupanga anapeza chisomo m'chipululu; Israele, muja anakapuma.


Akazi anu, ana anu, ndi zoweta zanu zikhale m'dzikoli anakuninkhani Mose, tsidya lino la Yordani; koma inu muoloke okonzeka kunkhondo pamaso pa abale anu, ngwazi zonse, ndi kuwathandiza;


Ndipo Yehova anawapatsa mpumulo pozungulira ponse, monga mwa zonse adalumbirira makolo ao; ndipo pamaso pao sipanaime munthu mmodzi wa adani ao onse; Yehova anapereka adani ao onse m'manja mwao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa