Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yoswa 1:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo Yoswa anati kwa Arubeni, ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo Yoswa anati kwa Arubeni, ndi Agadi, ndi fuko la Manase logawika pakati, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndipo Yoswa adauza fuko la Rubeni ndi la Gadi ndi theka la fuko la Manase kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Koma Yoswa anawuza fuko la Rubeni, fuko la Gadi ndi theka la fuko la Manase kuti,

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 1:12
5 Mawu Ofanana  

Ndi abale ake ngwazi ndiwo zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi awiri, akulu a nyumba za makolo, amene mfumu Davide anaika akhale oyang'anira a Arubeni, ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase, pa zinthu zonse za Mulungu ndi zinthu za mfumu.


Ana a Rubeni, ndi a Gadi, ndi hafu la fuko la Manase, ngwazi, amuna akugwira chikopa ndi lupanga, ndi kuponya mivi, ozolowera nkhondo, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zinai mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi limodzi akutuluka kunkhondo.


Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase,


nanena nao, Mwasunga inu zonsezo anakulamulirani Mose mtumiki wa Yehova; mwamveranso mau anga m'zonse ndinakulamulirani inu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa