Yoswa 1:10 - Buku Lopatulika10 Pamenepo Yoswa analamulira akapitao a anthu, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pamenepo Yoswa analamulira akapitao a anthu, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pamenepo Yoswa adalamula atsogoleri a Aisraele naŵauza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsono Yoswa analamula atsogoleri a Aisraeli nawawuza kuti, Onani mutuwo |