Yona 4:7 - Buku Lopatulika7 Koma Mulungu anauikira mphanzi pakucha m'mawa mwake, ndiyo inadya msatsi, nufota. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma Mulungu anauikira mphanzi pakucha m'mawa mwake, ndiyo inadya msatsi, nufota. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Koma m'maŵa mwake mbandakucha, Mulungu adatuma mphanzi kuti ikadye msatsiwo, ndipo udafota. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma tsiku linalo mmawa, Mulungu anabweretsa mbozi imene inadya msatsiyo ndipo inafota. Onani mutuwo |