Yona 3:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yona nthawi yachiwiri, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yona nthawi yachiwiri, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adalankhula ndi Yona kachiŵiri, namuuza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo Yehova anayankhula ndi Yona kachiwiri kuti, Onani mutuwo |