Yona 2:5 - Buku Lopatulika5 Madzi anandizinga mpaka moyo wanga, madzi akuya anandizungulira, kayandeyande wa m'nyanja anandikulunga mutu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Madzi anandizinga mpaka moyo wanga, madzi akuya anandizungulira, kayandeyande wa m'nyanja anandikulunga mutu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Madzi adandiyesa m'khosi, nyanja yozama idandizungulira. Udzu wakayandeyande udandikwidzinga m'mutu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Madzi wondimiza anandichititsa mantha, nyanja yozama inandizungulira; udzu wa mʼmadzi zinakuta mutu wanga. Onani mutuwo |