Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yona 2:1 - Buku Lopatulika

1 Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wake ali m'mimba mwa nsombayo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wake ali m'mimba mwa nsombayo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tsono Yona ali m'mimba mwa chinsomba chija, adayamba kutama Chauta mopemba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Yona ali mʼmimba mwa chinsomba chija anapemphera kwa Yehova Mulungu wake.

Onani mutuwo Koperani




Yona 2:1
12 Mawu Ofanana  

Ndipo kudzakhala kuti uzikamwa mumtsinje, ndipo ndalamulira makwangwala kukudyetsa kumeneko.


Angakhale andipha koma ndidzamlindira; komanso ndidzaumirira mayendedwe anga pamaso pake.


Ndipo undiitane tsiku la chisautso, ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.


Adzandifuulira Ine ndipo ndidzamyankha; kunsautso ndidzakhala naye pamodzi; ndidzamlanditsa, ndi kumchitira ulemu.


Yehova, iwo adza kwa Inu movutika, iwo anathira pemphero, muja munalikuwalanga.


Ndidzamuka ndi kubwerera kunka kumalo kwanga, mpaka adzavomereza kupalamula kwao, nafunafuna nkhope yanga; m'msauko mwao adzandifunafuna mwachangu.


Kodi wina wa inu akumva zowawa? Apemphere. Kodi wina asekera? Aimbire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa