Yona 1:13 - Buku Lopatulika13 Koma amunawo anapalasa kubwerera kumtunda, koma sanathe; pakuti namondwe wa panyanja anakulakula mokomana nao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Koma amunawo anapalasa kubwerera kumtunda, koma sanathe; pakuti namondwe wa panyanja anakulakula mokomana nao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Amalinyero adayesetsa kupalasa kwambiri kuti abwerere ku mtunda, koma adalephera ndithu, poti mafunde ankakwererakwerera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Komabe oyendetsa sitimayo anayesetsa kupalasa kwambiri kuti abwerere ku mtunda koma analephera ndithu poti nyanja inawinduka kwambiri kuposa poyamba paja Onani mutuwo |