Yona 1:11 - Buku Lopatulika11 Tsono anati kwa iye, Tichitenji nawe, kuti nyanja itichitire bata? Popeza namondwe anakulakulabe panyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Tsono anati kwa iye, Tichitenji nawe, kuti nyanja itichitire bata? Popeza namondwe anakulakulabe panyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono adamufunsa kuti, “Kodi tikuchite chiyani kuti nyanjayi ikhale bata?” M'menemo nkuti namondwe uja akukulirakulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Namondwe ananka nakulirakulirabe pa nyanjapo. Tsono anamufunsa iye kuti, “Kodi tikuchite chiyani kuti nyanjayi ikhale bata?” Onani mutuwo |