Yohane 9:38 - Buku Lopatulika38 Koma iye anati, Ndikhulupirira, Ambuye; ndipo anamgwadira Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Koma iye anati, Ndikhulupirira, Ambuye; ndipo anamgwadira Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Iye adati, “Ambuye, ndikukhulupirira.” Atatero adamgwadira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Pamenepo munthuyo anati, “Ambuye, ndikukhulupirira,” ndipo anamulambira Iye. Onani mutuwo |