Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 9:33 - Buku Lopatulika

33 Ngati uyu sanachokere kwa Mulungu, sakadakhoza kuchita kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Ngati uyu sanachokera kwa Mulungu, sakadakhoza kuchita kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Munthu ameneyu akadapanda kuchokera kwa Mulungu, sakadatha konse kuchita kanthu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Ngati munthu uyu akanakhala wosachokera kwa Mulungu, palibe chimene Iye akanachita.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 9:33
4 Mawu Ofanana  

Iyeyu anadza kwa Yesu usiku, nati kwa Iye, Rabi, tidziwa kuti Inu ndinu mphunzitsi wochokera kwa Mulungu; pakuti palibe munthu akhoza kuchita zizindikiro zimene Inu muchita, ngati Mulungu sakhala naye.


Ena pamenepo mwa Afarisi ananena, Munthu uyu sachokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata. Koma ena ananena, Munthu ali wochimwa akhoza bwanji kuchita zizindikiro zotere? Ndipo panali kutsutsana mwa iwo.


Kuyambira pachiyambi sikunamveke kuti wina anatsegulira maso munthu wosaona chibadwire.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa