Yohane 7:50 - Buku Lopatulika50 Nikodemo ananena kwa iwo, amene uja adadza kwa Iye kale, ali mmodzi wa iwo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Nikodemo ananena kwa iwo, amene uja adadza kwa Iye kale, ali mmodzi wa iwo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Tsono Nikodemo, mmodzi mwa Afarisi, yemwe uja amene kale adaapita kwa Yesu, adafunsa anzakewo kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Nekodimo, amene anapita kwa Yesu poyamba paja ndipo anali mmodzi wa iwo, anafunsa kuti, Onani mutuwo |