Yohane 6:65 - Buku Lopatulika65 Ndipo ananena, Chifukwa cha ichi ndinati kwa inu, kuti palibe munthu angathe kudza kwa Ine, koma ngati kupatsidwa kwa iye ndi Atate. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201465 Ndipo ananena, Chifukwa cha ichi ndinati kwa inu, kuti palibe munthu angathe kudza kwa Ine, koma ngati kupatsidwa kwa iye ndi Atate. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa65 Tsono adati, “Nchifukwa chake ndinakuuzani kuti palibe munthu amene angabwere kwa Ine ngati Atate sampatsa mphamvu zobwerera kwa Ine.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero65 Iye anapitiriza kunena kuti, “Ichi ndi chifukwa chake ndinakuwuzani kuti palibe wina angabwere kwa Ine pokhapokha Atate atamuthandiza.” Onani mutuwo |