Yohane 5:29 - Buku Lopatulika29 nadzatulukira, amene adachita zabwino, kukuuka kwa moyo; koma amene adachita zoipa kukuuka kwa kuweruza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 nadzatulukira, amene adachita zabwino, kukuuka kwa moyo; koma amene adachita zoipa kukuuka kwa kuweruza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Anthu amene adachita zabwino, adzauka kuti akhale ndi moyo, koma amene adachita zoipa, adzauka kuti azengedwe mlandu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 ndi kutuluka. Iwo amene anachita zabwino adzauka ndi kupita ku moyo wosatha ndipo amene anachita zoyipa adzauka ndi kupita ku chilango chamuyaya. Onani mutuwo |