Yohane 21:24 - Buku Lopatulika24 Yemweyu ndiye wophunzira wakuchita umboni za izi, ndipo analembera izi; ndipo tidziwa kuti umboni wake ndi woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Yemweyu ndiye wophunzira wakuchita umboni za izi, ndipo analembera izi; ndipo tidziwa kuti umboni wake ndi woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Ameneyo ndiye wophunzira uja amene akuchitira umboni zimene zidachitikazo, ndipo ndiye amene adazilemba. Tikudziŵa kuti umboni wakewo ngwoona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Uyu ndi wophunzira amene akuchitira umboni ndipo ndi amene analemba. Ife tidziwa kuti umboni wake ndi woona. Onani mutuwo |