Yohane 20:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo zizindikiro zina zambiri Yesu anazichita pamaso pa ophunzira ake, zimene sizinalembedwe m'buku ili; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo zizindikiro zina zambiri Yesu anazichita pamaso pa ophunzira ake, zimene sizinalembedwa m'buku ili; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Yesu adachitanso zizindikiro zina zambiri zozizwitsa pamaso pa ophunzira ake, zimene sizidalembedwe m'buku muno. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Yesu anachita zodabwitsa zambiri pamaso pa ophunzira ake zimene sizinalembedwe mʼbuku lino. Onani mutuwo |