Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 20:29 - Buku Lopatulika

29 Yesu ananena kwa iye, Chifukwa wandiona Ine, wakhulupirira; odala iwo akukhulupirira, angakhale sanaone.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Yesu ananena kwa iye, Chifukwa wandiona Ine, wakhulupirira; odala iwo akukhulupirira, angakhale sanaona.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Yesu adati, “Kodi wakhulupirira chifukwa wandiwona? Ngwodala amene amakhulupirira ngakhale sadaone.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Kenaka Yesu anamuwuza kuti, “Kodi wakhulupirira chifukwa wandiona Ine? Ndi odala amene amakhulupirira ngakhale asanaone.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:29
10 Mawu Ofanana  

Koma maso anu ali odala, chifukwa apenya; ndi makutu anu chifukwa amva.


Ndipo wodala ali iye amene anakhulupirira; chifukwa zidzachitidwa zinthu zimene Ambuye analankhula naye.


Tomasi anayankha nati kwa Iye, Ambuye wanga, ndi Mulungu wanga.


Pamenepo tsono analowanso wophunzira winayo, amene anayamba kufika kumanda, ndipo anaona, nakhulupirira.


Pamenepo Yesu anati kwa iye, Ngati simuona zizindikiro ndi zozizwa, simudzakhulupirira.


(Pakuti tiyendayenda mwa chikhulupiriro si mwa chionekedwe);


Koma chikhulupiriro ndicho chikhazikitso cha zinthu zoyembekezeka, chiyesero cha zinthu zosapenyeka.


Ndi chikhulupiriro anasiya Ejipito, wosaopa mkwiyo wa mfumu; pakuti anapirira molimbika, monga ngati kuona wosaonekayo.


Ndipo iwo onse adachitidwa umboni mwa chikhulupiriro, sanalandire lonjezanolo,


amene mungakhale simunamuone mumkonda; amene mungakhale simumpenya tsopano, pokhulupirira, mukondwera naye ndi chimwemwe chosaneneka, ndi cha ulemerero:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa