Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 20:24 - Buku Lopatulika

24 Koma Tomasi, mmodzi wa khumi ndi awiriwo, wotchedwa Didimo, sanakhale nao pamodzi, pamene Yesu anadza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Koma Tomasi, mmodzi wa khumi ndi awiriwo, wotchedwa Didimo, sanakhala nao pamodzi, pamene Yesu anadza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Mmodzi mwa ophunzira aja khumi ndi aŵiri, Tomasi (wotchedwa Didimo), sanali pamodzi ndi anzake pamene Yesu adaabwera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Koma Tomasi (otchedwa Didimo), mmodzi wa khumi ndi awiriwo, sanali ndi ophunzira pamene Yesu anabwera.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:24
9 Mawu Ofanana  

Filipo, ndi Bartolomeo; Tomasi, ndi Mateyu wamsonkho yo; Yakobo mwana wa Alifeyo, ndi Tadeyo;


Pakuti kumene kuli awiri kapena atatu asonkhanira m'dzina langa, ndili komweko pakati pao.


Pamenepo Tomasi, wotchedwa Didimo, anati kwa ophunzira anzake, Tipite ifenso kuti tikafere naye pamodzi.


Tomasi ananena ndi Iye, Ambuye, sitidziwa kumene munkako; tidziwa njira bwanji?


Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wotchedwa Didimo, ndi Natanaele wa ku Kana wa ku Galileya, ndi ana a Zebedeo, ndi awiri ena a ophunzira ake.


Yesu anayankha iwo, Kodi sindinakusankhani khumi ndi awiri, ndipo mwa inu mmodzi ali mdierekezi?


Koma adanena za Yudasi, mwana wa Simoni Iskariote, pakuti iye ndiye amene akampereka Iye, ali mmodzi wa khumi ndi awiri.


osaleka kusonkhana kwathu pamodzi, monga amachita ena, komatu tidandaulirane, ndiko koposa monga momwe muona tsiku lilikuyandika.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa