Yohane 20:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo pamene anati ichi anawapumira, nanena nao, Landirani Mzimu Woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo pamene anati ichi anawapumira, nanena nao, Landirani Mzimu Woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Pambuyo pake adaŵauzira mpweya nati, “Landirani Mzimu Woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndi mawu amenewo Iye anawapumira ndipo anati, “Landirani Mzimu Woyera. Onani mutuwo |