Yohane 20:18 - Buku Lopatulika18 Maria wa Magadala anapita, nalalikira kwa ophunzirawo, kuti, Ndaona Ambuye; ndi kuti ananena izi kwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Maria wa Magadala anapita, nalalikira kwa ophunzirawo, kuti, Ndaona Ambuye; ndi kuti ananena izi kwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Maria wa ku Magadalayo adapita, nakauza ophunzira aja kuti, “Ndaŵaona Ambuye,” ndipo adaŵakambira zimene Ambuyewo adaamtuma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mariya wa ku Magadala anapita kwa ophunzira ndi uthenga wakuti, “Ndamuona Ambuye!” Iye anawawuza iwo kuti Yesu ananena zinthu izi kwa iye. Onani mutuwo |