Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 20:14 - Buku Lopatulika

14 M'mene adanena izi, anacheuka m'mbuyo, naona Yesu ali chilili, ndipo sanadziwe kuti ndiye Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 M'mene adanena izi, anacheuka m'mbuyo, naona Yesu ali chilili, ndipo sanadziwa kuti ndiye Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Atanena zimenezi adacheuka, naona Yesu ataimirira pomwepo, koma sadamzindikire kuti ndi Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Atanena izi, iye anatembenuka ndipo anaona Yesu atayima potero koma iye sanazindikire kuti anali Yesu.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 20:14
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Yosefe anazindikira abale ake, koma iwo sanamzindikire iye.


Ndipo onani, Yesu anakomana nao, nanena, Tikuoneni. Ndipo iwo anadza, namgwira Iye mapazi ake, namgwadira.


Ndipo zitatha izi, anaonekanso Iye m'maonekedwe ena kwa awiri a iwo alikuyenda kupita kumidzi.


Ndipo pamene Iye adauka mamawa tsiku loyamba la sabata, anayamba kuonekera kwa Maria wa Magadala, amene Iye adamtulutsira ziwanda zisanu ndi ziwiri.


Koma maso ao anagwidwa kuti asamzindikire Iye.


Ndipo maso ao anatseguka, ndipo anamzindikira Iye; ndipo anawakanganukira Iye, nawachokera.


Koma Iye anapyola pakati pao, nachokapo.


Koma pakuyamba kucha, Yesu anaimirira pambali pa nyanja, komatu ophunzirawo sanadziwe kuti ndiye Yesu.


Pamenepo anatola miyala kuti amponye Iye; koma Yesu anabisala, natuluka mu Kachisi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa