Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yohane 19:37 - Buku Lopatulika

37 Ndipo linenanso lembo lina, Adzayang'ana pa Iye amene anampyoza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 Ndipo linenanso lembo lina, Adzayang'ana pa Iye amene anampyoza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Ndipo penanso Malembo akuti, “Anthu azidzamuyang'ana amene iwo adamubaya.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 ndi monga lemba linanso linena, “Iwo adzayangʼana Iye amene iwo anamubaya.”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 19:37
3 Mawu Ofanana  

Ndipo ndidzatsanulira pa nyumba ya Davide, ndi pa okhala mu Yerusalemu, mzimu wa chisomo ndi wakupembedza; ndipo adzandipenyera Ine amene anandipyoza; nadzamlira ngati munthu alira mwana wake mmodzi yekha, nadzammvera zowawa mtima, monga munthu amvera zowawa mtima mwana wake woyamba.


Taonani, adza ndi mitambo; ndipo diso lililonse lidzampenya Iye, iwonso amene anampyoza; ndipo mafuko onse a padziko adzamlira Iye. Terotu. Amen.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa