Yohane 19:32 - Buku Lopatulika32 Chifukwa chake anadza asilikali nathyola miyendo ya woyambayo, ndi ya winayo wopachikidwa pamodzi ndi Iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Chifukwa chake anadza asilikali nathyola miyendo ya woyambayo, ndi ya winayo wopachikidwa pamodzi ndi Iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tsono asilikali adabwera, nathyola miyendo ya mmodzi mwa aŵiri aja amene adaapachikidwa pamodzi ndi Yesu. Adateronso ndi mnzake uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Chifukwa chake asilikali anabwera ndi kuthyola miyendo ya munthu oyamba amene anapachikidwa ndi Yesu ndipo kenaka ya winayo. Onani mutuwo |