Yohane 19:25 - Buku Lopatulika25 Koma pamtanda wa Yesu anaimirira amake, ndi mbale wa amake, Maria, mkazi wa Kleopa, ndi Maria wa Magadala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma pamtanda wa Yesu anaimirira amake, ndi mbale wa amake, Maria, mkazi wa Kleopa, ndi Maria wa Magadala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Pafupi ndi mtanda wa Yesu padaaimirira amai ake, ndi mbale wa amai akewo, Maria mkazi wa Kleopa, ndi Maria wa ku Magadala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pafupi ndi mtanda wa Yesu panayima amayi ake, mngʼono wa amayi ake, Mariya mkazi wa Kaliyopa ndi Mariya wa ku Magadala. Onani mutuwo |