Yohane 18:39 - Buku Lopatulika39 Koma muli nao makhalidwe, akuti ndimamasulira inu mmodzi pa Paska; kodi mufuna tsono kuti ndimasulire inu mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Koma muli nao makhalidwe, akuti ndimamasulira inu mmodzi pa Paska; kodi mufuna tsono kuti ndimasulire inu mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Koma potsata chizoloŵezi chanu, pa nthaŵi ya chikondwerero cha Paska ndimakumasulirani mkaidi mmodzi. Tsono kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayudayi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Koma ndi mwambo wanu kuti pa nthawi ya Paska, ine ndikumasulireni wamʼndende mmodzi. Kodi mufuna ndikumasulireni ‘Mfumu ya Ayuda?’ ” Onani mutuwo |