Yohane 18:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo Pilato anati kwa iwo, Mumtenge Iye inu, ndi kumweruza Iye monga mwa chilamulo chanu. Ayuda anati kwa iye, Tilibe ulamuliro wakupha munthu aliyense; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo Pilato anati kwa iwo, Mumtenge Iye inu, ndi kumweruza Iye monga mwa chilamulo chanu. Ayuda anati kwa iye, Tilibe ulamuliro wakupha munthu aliyense; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Choncho Pilato adaŵauza kuti, “Mtengenitu tsono inuyo, mukamuweruze potsata malamulo anu.” Koma Ayudawo adati, “Ife sitiloledwa kupha munthu ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Pilato anati, “Mutengeni inu eni ake ndi kumuweruza Iye monga mwa malamulo anu.” Ayuda anatsutsa nati, “Koma tilibe ulamuliro wakupha aliyense.” Onani mutuwo |