Yohane 18:29 - Buku Lopatulika29 Chifukwa chake Pilato anatulukira kunja kwa iwo, nati, Chifukwa chanji mwadza nacho cha munthu uyu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Chifukwa chake Pilato anatulukira kunja kwa iwo, nati, Chifukwa chanji mwadza nacho cha munthu uyu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Motero Pilato adatulukira kwa iwo naŵafunsa kuti, “Mwampeza cholakwa chanji munthuyu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Choncho Pilato anatuluka napita kwa iwo ndipo anati, “Kodi ndi milandu yanji imene mukumuzenga munthu uyu?” Onani mutuwo |